Numbers 1:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Isakara, adapezeka kuti ali 54,400.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
owerengedwa ao a fuko la Isakara, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zinai kudza mazana anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Isakara chinali 54,400.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
owerengedwa ao a pfuko la lsakara, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zinai kudza mazana anai.