Numbers 1:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe ndi Aroni muŵerenge anthu, gulu ndi gulu, a zaka makumi aŵiri ndi opitirirapo, ndiye kuti anthu onse a ku Israele amene angathe kumenya nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwe ndi Aroni muwawerenge monga mwa magulu ao, onse m'Israele akutuluka ku nkhondo, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe ndi Aaroni mwawerenge mwa magulu awo mu Israeli, amuna onse a zaka makumi awiri zakubadwa ndi opitirirapo omwe angathe kugwira ntchito ya usilikali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwe ndi Aroni muwawerenge monga mwa magulu ao, onse m'Israyeli akuturuka kunkhondo, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu,