Numbers 1:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Zebuloni, adapezeka kuti ali 57,400.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
owerengedwa ao a fuko la Zebuloni, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zisanu ndi ziwiri kudza mazana anai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Zebuloni chinali 57,400.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
owerengedwa ao a pfuko la Zebuloni, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zisanu ndi ziwiri kudza mazana anai.