Numbers 1:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Dani, adapezeka kuti ali 62,700.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
owerengedwa ao a fuko la Dani, ndiwo zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu ziwiri kudza mazana asanu ndi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Dani chinali 62,700.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
owerengedwa ao a pfuko la Dani, ndiwo zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu ziwiri kudza mazana asanu ndi awiri.