Numbers 1:45 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho amuna onse a mu Israele otha kumenya nkhondo, a zaka 20 ndi a zaka zopitirirapo, potsata banja la makolo ao,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero owerengedwa onse a ana a Israele monga mwa nyumba za makolo ao, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo m'Israele;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aisraeli onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali mʼgulu lankhondo la Israeli anawawerenga monga mwa mabanja awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero owerengedwa onse a ana a Israyeli monga mwa nyumba za makolo ao, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akuturukira kunkhondo m'Israyeli;