Numbers 1:47 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Alevi okha sadaŵaŵerengere kumodzi ndi enawo, potsata banja la makolo ao,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Alevi monga mwa fuko la makolo ao sanawerengedwe mwa iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mabanja a fuko la Levi okha sanawawerenge pamodzi ndi ena.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Alevi monga mwa pfuko la makolo ao sanawerengedwa mwa iwo.