Numbers 10:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa chaka chachiŵiri, mwezi wachiŵiri, tsiku la 20, mtambo udachoka pa chihema chaumboni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunachitika, chaka chachiwiri, mwezi wachiwiri, tsiku la makumi awiri la mweziwo, kuti mtambo unakwera kuchokera kwa Kachisi wa mboni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa chaka chachiwiri, mwezi wachiwiri, tsiku la 20, mtambo unachoka pamwamba pa chihema cha umboni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunacitika, caka caciwiri, mwezi waciwiri, tsiku la makumi awiri la mweziwo, kuti mtambo unakwera kucokera kwa kacisi wa mboni.