Numbers 10:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtsogoleri wa gulu la fuko la Isakara anali Netanele mwana wa Zuwara.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pa gulu la fuko la ana a Isakara panali Netanele mwana wa Zuwara.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtsogoleri wa gulu la fuko la Isakara anali Netanieli mwana wa Zuwara,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pa gulu la pfuko la ana a Isakara panali Netaneli mwana wa Zuwara.