Numbers 10:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake otsata mbendera ya zithando za fuko la Rubeni adanyamuka m'magulumagulu, ndipo mtsogoleri wa gulu lao anali Elizuri mwana wa Sedeuri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi a mbendera ya chigono cha Rubeni, anayenda monga mwa magulu ao; ndipo pa gulu lake anayang'anira Elizuri mwana wa Sedeuri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka magulu a msasa wa fuko la Rubeni ananyamuka potsatira mbendera yawo. Mtsogoleri wawo anali Elizuri mwana wa Sedeuri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi a mbendera ya cigono ca Rubeni, anayenda monga mwa magulu ao; ndipo pa gulu lace anayang'anira Elizuri mwana wa Sedeuri.