Numbers 10:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtsogoleri wa gulu la Asimeoni anali Selumiele mwana wa Zurishadai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pa gulu la fuko la ana a Simeoni anayang'anira Selumiele mwana wa Zurishadai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtsogoleri wa fuko la Simeoni anali Selumieli mwana wa Zurisadai,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pa gulu la pfuko la ana a Simeoni anayang'anira Selumiyeli mwana wa Zurisadai.