Numbers 10:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Otsata mbendera ya zithando za fuko la Efuremu adanyamuka m'magulumagulu, ndipo mtsogoleri wa gulu lao anali Elisama mwana wa Amihudi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anayenda a mbendera ya chigono cha ana a Efuremu, monga mwa magulu ao; ndi pa gulu lake anayang'anira Elisama mwana wa Amihudi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Magulu a msasa wa Aefereimu anatsatira potsatira mbendera yawo. Elisama mwana wa Amihudi ndiye anali mtsogoleri wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anayenda a mbendera ya cigono ca ana a Efraimu, monga mwa magulu ao; ndi pa gulu lace anayang'anira Elizama mwana wa Amihudi.