Numbers 10:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtsogoleri wa gulu la fuko la Manase anali Gamaliele mwana wa Pedazuri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pa gulu la fuko la ana a Manase anayang'anira Gamaliele mwana wa Pedazuri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gamalieli mwana wa Pedazuri ndiye anali mtsogoleri wa fuko la Manase.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pa gulu la pfuko la ana a Manase anayang'anira Gamaliyeli mwana wa Pedazuri.