Numbers 10:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtsogoleri wa fuko la Abenjamini anali Abidani mwana wa Gideoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pa gulu la fuko la ana a Benjamini anayang'anira Abidani mwana wa Gideoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abidani mwana wa Gideoni ndiye anali mtsogoleri wa mtundu wa Benjamini.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pa gulu la pfuko la ana a Benjamini anayang'anira Abidana mwana wa Gideoni.