Numbers 10:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtsogoleri wa gulu la fuko la Asere anali Pagiyele mwana wa Okarani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pa gulu la fuko la ana a Asere anayang'anira Pagiyele mwana wa Okarani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pagieli mwana wa Okirani ndiye anali mtsogoleri wa fuko la Aseri,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pa gulu la pfuko la ana a Aseri anayang'anira Pagiyeli mwana wa Okirani.