Numbers 10:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtsogoleri wa gulu la fuko la Nafutali anali Ahira mwana wa Enani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pa gulu la fuko la ana a Nafutali anayang'anira Ahira mwana wa Enani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo mtsogoleri wa mtundu wa Nafutali anali Ahira mwana wa Enani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pa gulu la pfuko la ana a Nafitali anayang'anira Ahira mwana wa Enani.