Numbers 10:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Umenewu ndiwo mndandanda wa kayendedwe ka Aisraele, pamene ankanyamuka ulendo wao m'magulumagulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero maulendo a ana a Israele anakhala monga mwa magulu ao; nayenda ulendo wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Umenewu ndiwo unali mndandanda wa kayendedwe ka magulu a Aisraeli pamene ankanyamuka ulendo wawo mʼmagulumagulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero maulendo a ana a Israyeli anakhala monga mwa magulu ao; nayenda ulendowao.