Numbers 10:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtambo wa Chauta unkaŵaphimba masana, nthaŵi iliyonse pamene ankanyamuka pamahemapo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mtambo wa Yehova unali pamwamba pao msana, pakuyenda iwo kuchokera kuchigono.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtambo wa Yehova unkawaphimba masana pamene ankasamuka pa misasa yawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mtambo wa Yehova unali pamwamba pao msana, pakuyenda iwo kucokera kucigono.