Numbers 10:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtambowo ukaima, Mose ankati, “Inu Chauta, bwererani kwa Aisraele anu amene ali zikwi zosaŵerengeka.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi pakupumula ili anati, Bwerani Yehova kwa zikwizikwi za Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pamene likupumula, ankanena kuti, “Bwererani, Inu Yehova, ku chinamtindi cha Aisraeli.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi pakupumula ili anati, Bwerani Yehova kwa zikwi zikwi za Israyeli.