Numbers 10:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukaliza lipenga lochenjeza, anthu a m'mahema akuvuma ayambepo ulendo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukaliza chokweza ayende a m'zigono za kum'mawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akaliza lipenga lochenjeza, misasa yomwe ili kummawa iyambe kusamuka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukaliza cokweza, ayende a m'zigono za kum'mawa.