Numbers 11:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuchokera ku Mandaankhuliko, anthu adapita ku Hazeroti, ndipo adakhala komweko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuchokera ku Kibroti-Hatava anthuwo anayenda kunka ku Hazeroti; nakhala ku Hazeroti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuchoka pa Kibiroti Hatava anthuwo anayenda kupita ku Heziroti ndipo anakhala kumeneko kwa kanthawi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kucokera ku Kibiroti Hatava anthuwo anayenda kumka ku Hazeroti; nakhala ku Hazeroti.