Numbers 11:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma tsopano mphamvu zathu zatha, ndipo sitikuwona kanthu kena kakudya koma mana basi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma tsopano moyo wathu waphwa; tilibe kanthu pamaso pathu koma mana awa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma tsopano chilakolako chathu chatha. Sitikuona kanthu kena kakudya koma mana basi!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma tsopano moyo wathu waphwa; tiribe kanthu pamaso pathu koma mana awa.