Numbers 12:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Aroni adauza Mose kuti, “Mbuyanga, musatilange chifukwa choti tachimwa, ndipo tachita zopusa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Aroni anati kwa Mose, Mfumu yanga, musatiikiretu kuchimwa kumene tapusa nako, ndi kuchimwa nako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo Aaroni anawuza Mose kuti, “Pepani mbuye wanga, musatilange chifukwa cha tchimo limene tachita mopusa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Aroni anati kwa Mose, Mfumu yanga, musatiikiretu kucimwa kumene tapusa nako, ndi kucimwa nako.