Numbers 14:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzaŵapha ndi mliri ndi kuŵalanda choloŵa chao, ndipo iwe ndidzakusandutsa mtundu waukulu ndi wamphamvu kupambana iwoŵa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzawakantha ndi mliri, ndi kuwachotsera cholowa chao, ndipo ndidzakusandutsa iwe mtundu wa anthu waukulu ndi wamphamvu koposa iwowa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzawakantha ndi mliri ndi kuwawononga. Koma ndidzakusandutsa iwe mtundu waukulu ndi wamphamvu kuposa iwo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzawakantha ndi mliri, ndi kuwacotsera colowa cao, ndipo ndidzakusandutsa iwe mtundu wa anthu waukuru ndi wamphamvu koposa iwowa.