Numbers 14:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Mose adayankha Chauta kuti, “Zimenezitu Aejipito adzazimva, pakuti ndinu amene mudaŵatulutsa anthu ameneŵa m'dziko la Ejipito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mose anati kwa Yehova, Pamenepo Aejipito adzamva; popeza munakweza anthu awa ndi mphamvu yanu kuwachotsa pakati pao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mose anati kwa Yehova, “Aigupto adzamva zimenezi! Mwa mphamvu yanu munawatulutsa anthu amenewa pakati pawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mose anati kwa Yehova, Pamenepo Aaigupto adzamva; popeza munakweza anthu awa ndi mphamvu yanu kuwacotsa pakati pao;