Numbers 14:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
‘Chauta waŵaphera m'chipululu anthuŵa, chifukwa choti sadathe kuŵaloŵetsa m'dziko limene adalumbira kuti adzaŵapatsa kuti likhale lao.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza Yehova sanakhoze kuwalowetsa anthu awa m'dziko limene anawalumbirira, chifukwa chake anawapha m'chipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
‘Yehova walephera kuwalowetsa anthuwo mʼdziko lomwe anawalonjeza molumbira, ndipo wawapha mʼchipululu.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza Yehova sanakhoza kuwalowetsa anthu awa m'dziko limene anawalumbirira, cifukwa cace anawapha m'cipululu.