Numbers 14:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Kalebe mtumiki wanga, chifukwa ali ndi mtima wosiyana ndi ena, ndipo wanditsata ndi mtima wonse, ndidzamloŵetsa m'dziko limene adapitamolo, ndipo zidzukulu zake zidzalandira dzikolo kuti likhale lao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma mtumiki wanga Kalebe, popeza anali nao mzimu wina, nanditsata monsemo, ndidzamlowetsa iyeyu m'dziko muja analowamo; ndi mbeu zake zidzakhala nalo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mtumiki wanga Kalebe, pakuti ali ndi mtima wosiyana ndi ena ndiponso amanditsatira ndi mtima wonse, ndidzamulowetsa mʼdziko limene anapitamolo ndipo zidzukulu zake zidzalandira dzikolo ngati cholowa chawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma mtumiki wanga Kalebi, popeza anali nao mzimu wina, nanditsata monsemo, ndidzamlowetsa iyeyu m'dziko muja analowamo; ndi mbeu zace zidzakhala nalo.