Numbers 14:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono popeza kuti Aamaleke ndi Akanani amakhala m'zigwa, maŵa mubwerere, muyambepo ulendo wopita ku chipululu, mudzere ku Nyanja Yofiira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Aamaleke ndi Akanani akhala m'chigwamo; tembenukani mawa, nimumke ulendo wanu kuchipululu, njira ya ku Nyanja Yofiira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo popeza kuti Aamaleki ndi Akanaani akukhala ku chigwa, mawa mubwerere ndipo mupite ku chipululu podzera ku Nyanja Yofiira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Aamaleki ndi Akanani akhala m'cigwamo; tembenukani mawa, nimumke ulendo wanu kucipululu, njira ya ku Nyanja Yofiira.