Numbers 14:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
palibe ndi mmodzi yemwe amene adzaloŵe m'dziko limene ndidalumbira kuti mudzaloŵamo, kupatula Kalebe mwana wa Yefune ndi Yoswa mwana wa Nuni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
simudzalowa inu m'dzikolo, ndinakwezapo dzanja langa kukukhalitsani m'mwemo, koma Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni ndiwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palibe ndi mmodzi yemwe mwa inu amene adzalowe mʼdziko lomwe ndinalumbira mokweza manja kuti likhale lanu, kupatula Kalebe mwana wa Yefune ndi Yoswa mwana wa Nuni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
simudzalowa inu m'dzikolo, ndinakwezapo dzanja langa kukukhalitsani m'mwemo, koma Kalebi mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni ndiwo.