Numbers 14:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mwa anthu amene adapita kukazonda dziko aja, Yoswa mwana wa Nuni ndi Kalebe mwana wa Yefune ndiwo adatsala amoyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yoswa mwana wa Nuni, ndi Kalebe mwana wa Yefune, anakhala ndi moyo mwa amuna aja adamukawo kukazonda dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwa anthu amene anakaona dzikolo, Yoswa mwana wa Nuni ndi Kalebe mwana wa Yefune ndi okhawo amene anapulumuka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yoswa mwana wa Nuni, ndi Kalebi mwana wa Yefune, anakhala ndi moyo mwa amuna aja adamukawo kukazonda dziko.