Numbers 14:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumeneko Aamaleke ndi Akanani ali m'tsogolo mwanu, ndipo mudzaphedwa pa khondo. Chauta sadzakhala nanu, chifukwa choti mwaleka kumtsata.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Aamaleke ndi Akanani ali komweko patsogolo panu, ndipo mudzagwa ndi lupanga; popeza mwabwerera m'mbuyo osatsata Yehova, chifukwa chake Yehova sadzakhala nanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chifukwa kumeneko mukakumana ndi Aamaleki ndi Akanaani. Popeza mwaleka kutsata Yehova, Iyeyo sadzakhala nanu ndipo mudzaphedwa ndi lupanga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Aamaleki ndi Akanani ali komweko patsogolo panu, ndipo mudzagwa ndi lupanga; popeza mwabwerera m'mbuyo osatsata Yehova, cifukwa cace Yehova sadzakhala nanu.