Numbers 14:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mose ndi Aroni adadziponya pansi pamaso pa mpingo wonse wa Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Mose ndi Aroni anagwa nkhope pansi pamaso pa msonkhano wonse wa khamu la ana a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Mose ndi Aaroni anadzigwetsa pansi chafufumimba pamaso pa Aisraeli onse omwe anasonkhana pamenepo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Mose ndi Aroni anagwa nkhope pansi pamaso pa msonkhano wonse wa khamu la ana a Israyeli.