Numbers 14:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adauza mpingo wonse wa Aisraele uja kuti, “Dziko limene tidakalizondalo ndi labwino kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nanena ndi khamu lonse la ana a Israele, nati, Dziko tapitamo kulizonda, ndilo dziko lokometsetsa ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo anati kwa gulu lonse la Aisraeli, “Dziko limene tinakayendamo ndi kuliona ndi labwino kwambiri zedi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nanena ndi khamu lonse la ana a Israyeli, nati, Dziko tapitamo kulizonda, ndilo dziko lokometsetsa ndithu.