Numbers 15:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Umu ndimo m'mene zidzachitikire ndi ng'ombe yamphongo iliyonse, kapena nkhosa yamphongo, kapena mwanawankhosa aliyense kapena mwanawambuzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kudzatero ndi ng'ombe iliyonse, kapena nkhosa yamphongo iliyonse, kapena mwanawankhosa aliyense, kapena mwanawambuzi aliyense.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngʼombe yayimuna iliyonse kapena nkhosa yayimuna iliyonse, mwana wankhosa aliyense kapena mbuzi yayingʼono, zizikonzedwa motere.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kudzatero ndi ng'ombe iri yonse, kapena nkhosa yamphongo iri yonse, kapena mwana wa nkhosa ali yense, kapena mwana wa mbuzi ali yense.