Numbers 15:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zingachuluke chotani nyama zoperekedwazo, muchite choncho ndi nyama iliyonse, mpaka zonse kutha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga mwa kuwerenga kwake kwa izi muzikonza, muzitero ndi yonse monga mwa kuwerenga kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale zingachuluke chotani, chitani izi kwa iliyonse ya nyamazo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga mwa kuwerenga kwace kwa izi muzikonza, muzitero ndi yonse monga mwa kuwerenga kwace.