Numbers 15:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Uza Aisraele kuti, ‘Mukadzaloŵa m'dziko m'mene ndidzakufikitsani,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Pamene mulowa m'dziko limene ndilikukulowetsani,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yankhula ndi Aisraeli ndipo unene kuti, ‘Mukakalowa mʼdziko limene ndikukutengeraniko
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nena ndi ana a Israyeli, nuti nao, Pamene mulowa m'dziko limene ndirikukulowetsani,