Numbers 15:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Koma mwina mutha kulakwa mosadziŵa, osasunga malamulo onse amene Chauta adauza Mose,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo pamene mulakwa, osachita mau awa onse amene Yehova ananena ndi Mose;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Ndipo ngati muchimwa mosadziwa posasunga ena mwa malamulo awa amene Yehova wapereka kwa Mose,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo pamene mulakwa, osacita mau awa onse amene Yehova ananena ndi Mose;