Numbers 15:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
mpingo wonse wa Aisraele udzakhululukidwa pamodzi ndi mlendo yemwe amene akhala pakati pao, poti anthu onse adalakwa mosadziŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo khamu lonse la ana a Israele, adzakhululukidwa, ndi mlendo yemwe wakukhala pakati pao; popeza khamu lonse linachichita osati dala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gulu lonse la Aisraeli ndi alendo okhala pakati pawo adzakhululukidwa chifukwa anthu onsewo anachimwa mosadziwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo khamu lonse la ana a Israyeli, adzakhululukidwa, ndi mlendo yemwe wakukhala pakati pao; popeza khamu lonse linacicita osati dala.