Numbers 15:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ngati munthu mmodzi alakwa mosadziŵa, apereke mbuzi yaikazi ya chaka chimodzi kuti ikhale nsembe yopepesera machimo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akachimwa munthu mmodzi osati dala, abwere nayo mbuzi yamsoti ya chaka chimodzi, ikhale nsembe yauchimo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Koma ngati munthu mmodzi achimwa mosadziwa, ayenera kubweretsa mbuzi yayikazi ya chaka chimodzi kuti ikhale nsembe yopepesera machimo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akacimwa munthu mmodzi osati dala, abwere nayo mbuzi yamsoti ya caka cimodzi, ikhale nsembe yaucimo.