Numbers 15:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo mpingo udamtulutsira kunja kwa mahema munthuyo ndi kumupha pomponya miyala, monga momwe Chauta adaalamulira Mose.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo khamu lonse linamtulutsa kunja kwa chigono, ndi kumponya miyala, ndipo anafa; monga Yehova adauza Mose.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho gululo linamutengera kunja kwa msasa ndi kumupha pomugenda ndi miyala, monga momwe Yehova analamulira Mose.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo khamu lonse linamturutsa kunja kwa cigono, ndi kumponya miyala, ndipo anafa; monga Yehova adauza Mose.