Numbers 15:40 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho mudzakumbukira ndi kugwiritsa ntchito malamulo anga onse, mudzakhala oyera mtima pamaso pa Mulungu wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti mukumbukire ndi kuchita malamulo anga onse, ndi kukhala wopatulikira Mulungu wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Motero mudzakumbukira kumvera malamulo anga ndipo mudzakhala opatulikira a Mulungu wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti mukumbukile ndi kucita malamulo anga onse, ndi kukhala wopatulikira Mulungu wanu.