Numbers 16:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Chokani pakati pa mpingowu kuti ndiwononge onse nthaŵi imodzi.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Dzipatuleni pakati pa khamu lino, kuti ndiwathe m'kamphindi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Chokani pakati pa gulu ili kuti ndithetse mkanganowu kamodzinʼkamodzi.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Dzipatu, leni pakati pa khamu lino, kuti ndi wathe m'kamphindi.