Numbers 16:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero iwowo adaloŵa m'manda ali moyo, pamodzi ndi zinthu zao zonse. Nthaka idaŵatsekera pansi, motero adazimirira pakati pa msonkhano wonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chomwecho iwowa, ndi onse anali nao, anatsikira kumanda ali ndi moyo, ndi dziko linasunama pa iwo, ndipo anaonongeka pakati pa msonkhano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Analowa mʼmanda amoyo pamodzi ndi zonse zimene anali nazo. Nthaka inawatsekera ndi kuwawononga ndipo sanaonekenso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Comweco iwowa, ndi onse anali nao, anatsikira kumanda ali ndi moyo, ndi dziko linasunama pa iwo, ndipo anaonongeka pakati pa msonkhano.