Numbers 16:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo Aisraele onse amene anali pafupi adathaŵa, atamva anthuwo akulira. Ankati, “Tiyeni tithaŵe kuti nthakayi ingatimeze nafenso.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Aisraele onse akukhala pozinga pao anathawa pakumva kufuula kwao; pakuti anati, Lingatimeze dziko ifenso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atamva kulira kwawo, Aisraeli onse amene anali pafupi ndi anthuwo anathawa akufuwula kuti, “Nthaka imezanso ife!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Aisrayeli onse akukhala pozinga pao anathawa pakumva kupfuula kwao; pakuti anati, Lingatimeze dziko ifenso.