Numbers 16:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho wansembe Eleazara adatenga zofukizira zamkuŵa zija zimene adadzapereka anthu amene adapsa ndi moto aja. Adazisula chophimbira pa guwa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Eleazara wansembe anatenga mbale zofukiza zamkuwa, zimene anthu opsererawo adabwera nazo; ndipo anazisula zaphanthiphanthi zikhale chivundikiro cha guwa la nsembe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Eliezara, wansembe, anasonkhanitsa zofukizira zamkuwa zija zomwe anthu opsererawo anabwera nazo ndipo anazisula kuti zikhale zophimbira pa guwa lansembe,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Eleazara wansembe anatenga mbale zofukiza zamkuwa, zimene anthu opsererawo adabwera nazo; ndipo anazisula zaphanthiphanthi zikhale cibvundikilo ca guwala nsembe;