Numbers 16:41 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma m'maŵa mwake mpingo wonse wa Aisraele udaŵiringulira Mose ndi Aroni kuti, “Inu mwapha anthu a Chauta.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma m'mawa mwake khamu lonse la ana a Israele anadandaula pa Mose ndi Aroni, nati, Mwapha anthu a Yehova, inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsiku lotsatira, gulu lonse la Aisraeli linatsutsana ndi Mose ndi Aaroni. Iwo anati, “Inu mwapha anthu a Yehova.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma m'mawa mwace khamu lonse la ana a Israyeli anadandaula pa Mose ndi Aroni, nati, Mwapha anthu a Yehova, inu.