Numbers 16:45 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Choka pakati pa gulu la anthuli, kuti ndiŵaononge onse nthaŵi imodzi.” Aŵiriwo adadziponya pansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwerani kuchoka pakati pa khamu lino, kuti ndiwathe m'kamphindi. Pamenepo adagwa nkhope zao pansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Chokani pakati pa gulu la anthuwa kuti ndiwawononge kamodzinʼkamodzi.” Ndipo iwo anagwa pansi chafufumimba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kwerani kucoka pakati pa khamu lino, kuti ndiwathe m'kamphindi. Pamenepo adagwa nkhope zao pansi.