Numbers 18:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muzidyera ku malo opatulika kopambana. Mwamuna aliyense angathe kudyako. Zimenezi nzoyera kwa inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muzizidya izi monga zopatulika kwambiri; mwamuna yense adyeko; uziyese zopatulika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Muzidya zimenezo ngati zinthu zopatulika kwambiri; mwamuna aliyense adyeko. Uzitenge kukhala zopatulika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muzizidya izi monga zopatulikitsa; mwamuna yense adyeko; uziyese zopatulika.