Numbers 18:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chinthu chilichonse chimene anthu amapatulira Chauta m'dziko la Israele chikhale chanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zilizonse zoperekedwa chiperekere m'Israele ndi zako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Chilichonse mu Israeli chomwe chapatulidwira Yehova ndi chako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ziri zonse zoperekedwa ciperekere m'Israyeli ndi zako.