Numbers 18:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mungathe kuzidyera pa malo aliwonse, inuyo ndi a m'banja mwanu. Zimenezo ndi mphotho yanu chifukwa cha ntchito imene mumagwira m'chihema chamsonkhano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo muzidye pamalo ponse, inu ndi a pabanja panu; popeza ndizo mphotho yanu mwa ntchito yanu m'chihema chokomanako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu ndi a pa banja panu mungathe kudyera zimenezi paliponse chifukwa ndi malipiro a ntchito yanu ya ku tenti ya msonkhano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo muzidye pamalo ponse, inu ndi a pabanja panu; popeza ndizo mphotho yanu mwa nchito yanu m'cihema cokomanako.