Numbers 2:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mbali yakumwera kuzikhala mbendera ya zithando za fuko la Rubeni, m'magulumagulu. Mtsogoleri wa fuko la Rubeni ndi Elizuri mwana wa Sedeuri,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mbendera ya chigono cha Rubeni ikhale kumwera monga mwa makamu ao; ndipo kalonga wa ana a Rubeni ndiye Elizuri mwana wa Sedeuri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kummwera kudzakhala magulu a msasa wa Rubeni pamene pali mbendera yawo. Mtsogoleri wa gulu la Rubeni ndi Elizuri mwana wa Sedeuri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mbendera ya cigono ca Rubeni ikhale kumwera monga mwa makamu ao; ndipo kalonga wa ana a Rubeni ndiye Elizuri mwana wa Sedeuri.